Chivumbulutso 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngelo wa 5 analiza lipenga lake.+ Ndipo ndinaona nyenyezi imene inagwera padziko lapansi kuchokera kumwamba ija. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi wa dzenje lolowera kuphompho.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 143 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, ptsa. 17-1812/15/1988, ptsa. 12-13
9 Mngelo wa 5 analiza lipenga lake.+ Ndipo ndinaona nyenyezi imene inagwera padziko lapansi kuchokera kumwamba ija. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi wa dzenje lolowera kuphompho.+