Chivumbulutso 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyenyeziyo inatsegula dzenje lolowera kuphompholo ndipo utsi ngati wamungʼanjo yaikulu unatuluka mʼdzenjemo. Dzuwa komanso mpweya zinada+ ndi utsi wamʼdzenjewo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143-144 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 12-13
2 Nyenyeziyo inatsegula dzenje lolowera kuphompholo ndipo utsi ngati wamungʼanjo yaikulu unatuluka mʼdzenjemo. Dzuwa komanso mpweya zinada+ ndi utsi wamʼdzenjewo.