Chivumbulutso 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu utsiwo, munatuluka dzombe ndipo linabwera padziko lapansi.+ Dzombelo linapatsidwa ulamuliro wofanana ndi umene zinkhanira zapadziko lapansi zili nawo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143-144 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 12-13
3 Mu utsiwo, munatuluka dzombe ndipo linabwera padziko lapansi.+ Dzombelo linapatsidwa ulamuliro wofanana ndi umene zinkhanira zapadziko lapansi zili nawo.