Chivumbulutso 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzombelo linauzidwa kuti lisawononge zomera zapadziko lapansi, kapena chilichonse chobiriwira, kapena mtengo uliwonse, koma kuti livulaze anthu okhawo amene alibe chidindo cha Mulungu pachipumi pawo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 144-145, 147-148
4 Dzombelo linauzidwa kuti lisawononge zomera zapadziko lapansi, kapena chilichonse chobiriwira, kapena mtengo uliwonse, koma kuti livulaze anthu okhawo amene alibe chidindo cha Mulungu pachipumi pawo.+