Chivumbulutso 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzombelo linalinso ndi michira yomwe inali ndi mbola ngati zinkhanira. Mʼmichira yawoyo ndi mmene munali mphamvu zovulazira anthuwo kwa miyezi 5.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 146-148
10 Dzombelo linalinso ndi michira yomwe inali ndi mbola ngati zinkhanira. Mʼmichira yawoyo ndi mmene munali mphamvu zovulazira anthuwo kwa miyezi 5.+