-
Chivumbulutso 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiye angelo 4 amenewo anamasulidwa. Iwo anali okonzeka kuti pa ola, tsiku, mwezi ndi chaka chimenecho, aphe gawo limodzi mwa magawo atatu a anthu.
-