Chivumbulutso 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo chiwerengero cha gulu la asilikali okwera pamahatchi chinali 20 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande.* Chimenechi ndi chiwerengero chawo chimene ndinamva. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 149-153 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, tsa. 2912/15/1988, tsa. 13
16 Ndipo chiwerengero cha gulu la asilikali okwera pamahatchi chinali 20 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande.* Chimenechi ndi chiwerengero chawo chimene ndinamva.