-
Chivumbulutso 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mahatchi komanso amene anakwera pamahatchiwo ankaoneka chonchi mʼmasomphenyawo: Anavala zoteteza pachifuwa zofiira ngati moto, zabuluu ngati mwala wa huwakinto komanso zachikasu ngati sulufule. Mitu ya mahatchiwo inali ngati mitu ya mikango+ ndipo mʼkamwa mwawo munkatuluka moto, utsi ndi sulufule.
-