-
Chivumbulutso 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Gawo limodzi mwa magawo atatu a anthu anaphedwa ndi miliri itatu imene inatuluka mʼkamwa mwawo, yomwe ndi moto, utsi ndi sulufule.
-