-
Chivumbulutso 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mphamvu za mahatchiwo zinali mʼkamwa mwawo ndi mʼmichira yawo, chifukwa michira yawo inali ngati njoka ndipo inali ndi mitu. Michira imeneyi ankavulaza nayo anthu.
-