Chivumbulutso 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma anthu ena onse amene sanaphedwe ndi miliri imeneyi, sanalape ntchito za manja awo. Sanasiye kulambira ziwanda ndi mafano agolide, asiliva, akopa,* amwala ndi amtengo, amene sangathe kuona, kumva, kapena kuyenda.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:20 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 154
20 Koma anthu ena onse amene sanaphedwe ndi miliri imeneyi, sanalape ntchito za manja awo. Sanasiye kulambira ziwanda ndi mafano agolide, asiliva, akopa,* amwala ndi amtengo, amene sangathe kuona, kumva, kapena kuyenda.+