-
Chivumbulutso 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mʼdzanja lake, anali ndi mpukutu waungʼono wotambasula. Iye anaponda panyanja ndi phazi lake lakumanja koma ndi phazi lake lakumanzere anaponda pamtunda.
-