Chivumbulutso 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiye mabingu 7 aja atalankhula, ndinkafuna kulemba. Koma ndinamva mawu ochokera kumwamba+ akuti: “Usunge mwachinsinsi* zimene mabingu 7 amenewa alankhula ndipo usazilembe.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 157 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 19
4 Ndiye mabingu 7 aja atalankhula, ndinkafuna kulemba. Koma ndinamva mawu ochokera kumwamba+ akuti: “Usunge mwachinsinsi* zimene mabingu 7 amenewa alankhula ndipo usazilembe.”