Chivumbulutso 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho ndinapita kwa mngeloyo nʼkumuuza kuti andipatse mpukutu waungʼonowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa mʼmimba, koma mʼkamwa mwako ukhala wokoma ngati uchi.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160
9 Choncho ndinapita kwa mngeloyo nʼkumuuza kuti andipatse mpukutu waungʼonowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa mʼmimba, koma mʼkamwa mwako ukhala wokoma ngati uchi.”