Chivumbulutso 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma bwalo limene lili kunja kwa nyumba yopatulika yapakachisi ulisiye, usaliyeze chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina. Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, tsa. 3010/15/1988, tsa. 13 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 162-163
2 Koma bwalo limene lili kunja kwa nyumba yopatulika yapakachisi ulisiye, usaliyeze chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina. Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+