Chivumbulutso 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi+ komanso zoikapo nyale ziwiri+ ndipo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, tsa. 30 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 164
4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi+ komanso zoikapo nyale ziwiri+ ndipo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+