-
Chivumbulutso 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako mbonizo zinamva mawu ofuula kuchokera kumwamba akuziuza kuti: “Bwerani kuno.” Ndipo zinakwera kumwamba mumtambo adani awo akuona.
-