Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:15 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171-172, 176 Lambirani Mulungu, ptsa. 93-94 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 191/15/1990, ptsa. 19-204/1/1989, ptsa. 19-2012/15/1988, ptsa. 13-14 Kukambitsirana, tsa. 129
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+
11:15 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171-172, 176 Lambirani Mulungu, ptsa. 93-94 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 191/15/1990, ptsa. 19-204/1/1989, ptsa. 19-2012/15/1988, ptsa. 13-14 Kukambitsirana, tsa. 129