Chivumbulutso 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo akulu 24+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu aja, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo analambira Mulungu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 172-173
16 Ndipo akulu 24+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu aja, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo analambira Mulungu.