Chivumbulutso 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako kumwamba kunaoneka chizindikiro chachikulu. Kunaoneka mkazi+ atavala dzuwa ndipo mwezi unali pansi pa mapazi ake. Kumutu kwake kunali chisoti chachifumu chopangidwa ndi nyenyezi 12. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 177-178 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 117
12 Kenako kumwamba kunaoneka chizindikiro chachikulu. Kunaoneka mkazi+ atavala dzuwa ndipo mwezi unali pansi pa mapazi ake. Kumutu kwake kunali chisoti chachifumu chopangidwa ndi nyenyezi 12.