Chivumbulutso 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumwamba kunaoneka chizindikiro chinanso. Ndinaona chinjoka chachikulu chofiira+ chimene chinali ndi mitu 7 ndi nyanga 10 ndipo pamituyo panali zisoti zachifumu 7. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:3 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 178 Nsanja ya Olonda,9/1/2001, tsa. 64/1/1989, tsa. 20
3 Kumwamba kunaoneka chizindikiro chinanso. Ndinaona chinjoka chachikulu chofiira+ chimene chinali ndi mitu 7 ndi nyanga 10 ndipo pamituyo panali zisoti zachifumu 7.