Chivumbulutso 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mchira wake unakokolola gawo limodzi mwa magawo atatu a nyenyezi+ zakumwamba nʼkuzigwetsera padziko lapansi.+ Ndipo chinjokacho chinangoima pamaso pa mkazi+ amene anali atatsala pangʼono kubereka uja, kuti akabereka chidye mwana wakeyo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2018, tsa. 23 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 178-179
4 Mchira wake unakokolola gawo limodzi mwa magawo atatu a nyenyezi+ zakumwamba nʼkuzigwetsera padziko lapansi.+ Ndipo chinjokacho chinangoima pamaso pa mkazi+ amene anali atatsala pangʼono kubereka uja, kuti akabereka chidye mwana wakeyo.