Chivumbulutso 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri a chiwombankhanga chachikulu+ kuti aulukire kuchipululu, kumalo ake aja, kumene akuyenera kudyetsedwa kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi chinjoka chija.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:14 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 183-184
14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri a chiwombankhanga chachikulu+ kuti aulukire kuchipululu, kumalo ake aja, kumene akuyenera kudyetsedwa kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi chinjoka chija.+