-
Chivumbulutso 12:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma dziko lapansi linathandiza mkaziyo. Dzikolo linatsegula pakamwa pake nʼkumeza mtsinje umene chinjoka chija chinalavula kuchokera mʼkamwa mwake.
-