Chivumbulutso 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho chinjokacho chinakwiya ndi mkazi uja, moti chinapita kukachita nkhondo ndi mbadwa*+ zake zimene zinatsala, zomwe zimasunga malamulo a Mulungu ndipo zili ndi ntchito yochitira umboni za Yesu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, ptsa. 5-6, 16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 11-12, 183, 185-186, 279
17 Choncho chinjokacho chinakwiya ndi mkazi uja, moti chinapita kukachita nkhondo ndi mbadwa*+ zake zimene zinatsala, zomwe zimasunga malamulo a Mulungu ndipo zili ndi ntchito yochitira umboni za Yesu.+
12:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, ptsa. 5-6, 16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 11-12, 183, 185-186, 279