Chivumbulutso 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga wamʼmbali mwa nyanja. Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka mʼnyanja.+ Chinali ndi nyanga 10 ndi mitu 7. Panyanga yake iliyonse panali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, ptsa. 8-11, 14-182/15/2009, tsa. 44/1/2004, tsa. 44/1/1989, tsa. 2012/15/1988, tsa. 192/1/1986, ptsa. 5-6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-190
13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga wamʼmbali mwa nyanja. Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka mʼnyanja.+ Chinali ndi nyanga 10 ndi mitu 7. Panyanga yake iliyonse panali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.
13:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, ptsa. 8-11, 14-182/15/2009, tsa. 44/1/2004, tsa. 44/1/1989, tsa. 2012/15/1988, tsa. 192/1/1986, ptsa. 5-6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-190