Chivumbulutso 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinaona kuti mutu wake umodzi unkaoneka kuti unali utavulazidwa kwambiri. Koma balalo linapola+ ngakhale kuti chikanatha kufa nalo ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho chifukwa chochita nacho chidwi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 190-191 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 19-20
3 Ndinaona kuti mutu wake umodzi unkaoneka kuti unali utavulazidwa kwambiri. Koma balalo linapola+ ngakhale kuti chikanatha kufa nalo ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho chifukwa chochita nacho chidwi.
13:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 190-191 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 19-20