-
Chivumbulutso 13:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iwo analambira chinjoka chija chifukwa chinapereka ulamuliro kwa chilombo. Ndipo analambira chilombocho ndi mawu akuti: “Ndi ndani ali ngati chilombo ndipo ndi ndani angamenyane nacho?”
-