Chivumbulutso 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake nʼkumanyoza+ Mulungu. Chinkanyoza dzina lake, malo ake okhala komanso amene akukhala kumwamba.+
6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake nʼkumanyoza+ Mulungu. Chinkanyoza dzina lake, malo ake okhala komanso amene akukhala kumwamba.+