Chivumbulutso 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amene akukhala padziko lapansi adzachilambira. Kuchokera pamene dziko linakhazikitsidwa, anthu amenewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ wa Mwanawankhosa amene anaphedwa.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:8 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 3 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192
8 Anthu amene akukhala padziko lapansi adzachilambira. Kuchokera pamene dziko linakhazikitsidwa, anthu amenewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ wa Mwanawankhosa amene anaphedwa.+