Chivumbulutso 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati wina akuyenera kutengedwa kupita ku ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko. Aliyense wopha munthu ndi lupanga, nayenso adzaphedwa ndi lupanga.*+ Apa mʼpamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 192-193
10 Ngati wina akuyenera kutengedwa kupita ku ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko. Aliyense wopha munthu ndi lupanga, nayenso adzaphedwa ndi lupanga.*+ Apa mʼpamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+