14 Chilombocho chinasocheretsa anthu amene akukhala padziko lapansi chifukwa cha zizindikiro zimene chinaloledwa kuchita pamaso pa chilombo choyamba chija. Chinauzanso amene akukhala padziko lapansi kuti apange chifaniziro+ cha chilombo chimene chinali ndi bala la lupanga chija, koma sichinafe.+