Chivumbulutso 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya* kwa chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula komanso kuchititsa kuti onse amene akukana kulambira chifaniziro cha chilombocho aphedwe. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 19-20
15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya* kwa chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula komanso kuchititsa kuti onse amene akukana kulambira chifaniziro cha chilombocho aphedwe.
13:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 19-20