-
Chivumbulutso 14:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno ndinamva phokoso kuchokera kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba pogwiritsa ntchito azeze awo.
-