Chivumbulutso 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Apa mʼpamene oyerawo, amene akusunga malamulo a Mulungu ndi kutsatira chikhulupiriro+ cha Yesu, akufunika kupirira.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:12 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211
12 Apa mʼpamene oyerawo, amene akusunga malamulo a Mulungu ndi kutsatira chikhulupiriro+ cha Yesu, akufunika kupirira.”+