-
Chivumbulutso 14:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mngelo winanso anatuluka mʼnyumba yopatulika yapakachisi amene ali kumwamba, nayenso anali ndi chikwakwa chakuthwa.
-