Chivumbulutso 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mngeloyo anatsitsira chikwakwa chake padziko lapansi mwamphamvu nʼkumweta mpesa wapadziko lapansi. Kenako anauponya mʼchoponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 212-213, 215 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 21
19 Mngeloyo anatsitsira chikwakwa chake padziko lapansi mwamphamvu nʼkumweta mpesa wapadziko lapansi. Kenako anauponya mʼchoponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+