Chivumbulutso 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinaona chizindikiro china kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Chizindikiro chimenechi chinali angelo 7+ amene anali ndi miliri 7. Miliri imeneyi ndi yomaliza chifukwa ikamatha, mkwiyo wa Mulungu udzakhalanso utatha.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:1 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 215-216
15 Ndinaona chizindikiro china kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Chizindikiro chimenechi chinali angelo 7+ amene anali ndi miliri 7. Miliri imeneyi ndi yomaliza chifukwa ikamatha, mkwiyo wa Mulungu udzakhalanso utatha.+