Chivumbulutso 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinaona chinachake chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake+ ndi nambala ya dzina lake+ anali ataima pambali pa nyanja yagalasiyo, atanyamula azeze a Mulungu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 216-217
2 Kenako ndinaona chinachake chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake+ ndi nambala ya dzina lake+ anali ataima pambali pa nyanja yagalasiyo, atanyamula azeze a Mulungu.