Chivumbulutso 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo angelo 7 amene anali ndi miliri 7+ aja anatuluka kumalo opatulikawo, atavala zovala zoyera ndi zowala komanso atamanga malamba agolide pazifuwa zawo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219
6 Ndipo angelo 7 amene anali ndi miliri 7+ aja anatuluka kumalo opatulikawo, atavala zovala zoyera ndi zowala komanso atamanga malamba agolide pazifuwa zawo.