Chivumbulutso 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno mmodzi wa angelo 4 aja anapereka kwa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7 zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo mpaka kalekale. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219
7 Ndiyeno mmodzi wa angelo 4 aja anapereka kwa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7 zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo mpaka kalekale.