Chivumbulutso 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 219-220
8 Mʼmalo opatulikawo munadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa mʼmalo opatulikawo mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.