Chivumbulutso 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 chifukwa iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri+ ndipo inu mwawapatsa magazi kuti amwe.+ Iwo akuyeneradi kulandira chiweruzo chimenechi.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30-31, 224-225
6 chifukwa iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri+ ndipo inu mwawapatsa magazi kuti amwe.+ Iwo akuyeneradi kulandira chiweruzo chimenechi.”+