-
Chivumbulutso 16:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anthu anapsa ndi kutentha kwakukulu. Koma iwo ananyoza dzina la Mulungu, amene ali ndi ulamuliro pa miliri imeneyi ndipo sanalape nʼkumupatsa ulemerero.
-