Chivumbulutso 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkaziyo anavala zovala zapepo+ ndi zofiira kwambiri ndipo anadzikongoletsa ndi golide, miyala yamtengo wapatali ndiponso ngale.+ Mʼdzanja lake, anali ndi kapu yagolide yodzaza ndi zonyansa ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi chiwerewere* chake. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-245 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, ptsa. 12-134/1/1989, ptsa. 5-6
4 Mkaziyo anavala zovala zapepo+ ndi zofiira kwambiri ndipo anadzikongoletsa ndi golide, miyala yamtengo wapatali ndiponso ngale.+ Mʼdzanja lake, anali ndi kapu yagolide yodzaza ndi zonyansa ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi chiwerewere* chake.
17:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-245 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, ptsa. 12-134/1/1989, ptsa. 5-6