Chivumbulutso 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye mngelo uja anandifunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi+ ameneyu komanso cha chilombo chimene wakwerapo, chimene chili ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 246-247 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, ptsa. 13-14
7 Ndiye mngelo uja anandifunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi+ ameneyu komanso cha chilombo chimene wakwerapo, chimene chili ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+