-
Chivumbulutso 17:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Chilombo chimene waona, chinalipo, koma panopa kulibe, komabe chatsala pangʼono kutuluka kuphompho,+ ndipo chipita kuchiwonongeko. Anthu amene akukhala padziko lapansi, amene mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa, adzadabwa kwambiri akadzaona kuti chilombocho chinalipo, panopa kulibe, koma chidzakhalaponso.
-