14 Iwo adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma chifukwa chakuti iye ndi Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, omwe ndi osankhidwa mwapadera ndiponso okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+