Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo uja anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, magulu a anthu, mayiko komanso zilankhulo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:15 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 256 Galamukani!,11/8/1996, ptsa. 5-6
15 Mngelo uja anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, magulu a anthu, mayiko komanso zilankhulo.+