Chivumbulutso 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mubwezereni zofanana ndi zimene iye anachitira ena.+ Mubwezereni kuwirikiza kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ Mʼkapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho kuwirikiza kawiri.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266
6 Mubwezereni zofanana ndi zimene iye anachitira ena.+ Mubwezereni kuwirikiza kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ Mʼkapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho kuwirikiza kawiri.+